madradra - yobezani lyrics
[intro]
[classic!]
[ace*tee on the beat]
[eyo mayne!]
wasup bruh!
[who is this jesus you keep rapping about, mayne?]
[ndi ndani kwenikweni aise?]
alright, so you wanna know him?
[yeah, mayne!]
okay, listen!
[verse 1]
za iye un*z*mvapo kale
koma sumazitengera umangoti zikhale
zimak*mvekera mwa nthano, no wonder you doubt it
mtima unawuumitsa, you don’t wanna be about it
eeh! i relate ‘cause nane n’nali choncho
before the truth hit my heart n’nali bonzo
and religion made it worse, inali smoko
n’kona nd*nkadzimva u atheist ngati dolo
komano n’tak*mana naye man
amene ndin’kati ndi myth
maso anatseguka ndinati ndimutsate man
truth is who i’m rolling with
nde pano palibe angandinamize adha
zi philosophies of men sizingandihite adha
got the living word in me, sentence singafike adha
olo atandijaja bola i truly know him adha
[chorus]
dziko limam’kana koma silimadziwa man
[silimadziwa man]
kuti iye si munthu wamba
ndi namalenga samafеra opinions of man
[opinions of man]
ndipo siudzamva
‘cause iye ndi madradra, dradra
[dradra, dradra]
and enawa ndi ma bluntеr, blunter
[blunter, blunter]
[verse 2]
let’s go deeper now
i’m just being a vessel, the spirit is your teacher now
ngati golden hour, you gonna have the picture now
of who christ really is mpaka umudziwa nawo
yeah! ey, iye n’namalenga
he’s uncreated nde creation imalenga
and he sustains us ndi zomwe amanena
ndi mwa iye yekha momwe ife tipeza worth bruh
nde zija unamva zoti anadzatifera man
ndi zoona, sikuti n’zongopeka man
koma it’s a reality kwa tinadzipereka man
moona, he became our savior man
and we were made partakers of his sacrifice
moti tinafa naye, n’kuuka naye m’mandamo
n’kugonjetsa adani onse ndi chi landslide
palibiletu angapange raise madando
[chorus]
dziko limam’kana koma silimadziwa man
[silimadziwa man]
kuti iye si munthu wamba
ndi namalenga samafera opinions of man
[opinions of man]
ndipo siudzamva
‘cause iye ndi madradra, dradra
[dradra, dradra]
and enawa ndi ma blunter, blunter
[blunter, blunter]
[outro]
yeah, that’s it mayne. and just because man denies the deity of jesus christ it doesn’t mean kuti he stops being god, nah!
he is god and he doesn’t depend on man’s opinion about him. man has to know that jesus is supreme in power, glory, authority and importance
ndi madradra!
yeah, yobezani!
ndi madradra!
[ace*tee on the beat]
Random Song Lyrics :
- non ci posso credere//quando capisci - puntoteopunto lyrics
- epitaph - preripped lyrics
- adrenaline - 115tri lyrics
- speeding - laetho lyrics
- twominutes - xanadu lyrics
- start again - arata lyrics
- 2000's suite - atomic baby lyrics
- walking in god’s sunshine - the happy goodmans lyrics
- red dot - slicethroat lyrics
- danger (rag doll album) - the four seasons lyrics