nfumu - willz mr nyopole lyrics
no police in the house number
mr nyopole
ah jeremia kodi wakonka
mumati nsale nanda?
phat jams babe
pwee
[chorus ]
ma rapper, ana owa ngati afisi
yai samafika pa fupi
ngati upalauka upanga makwacha
anthu amati ndi nfiti, ndi nfiti
mponda matiki ndi mfwiti
nfumu, yai samazicha zicha nfumu
anthu ndiye amamucha nfumu
ngati wee kena kazi ndiwe nfumu
[verse 1]
bena asambila betasol
bena asambila mekako
bena asambila ch*nkondya
sandusa ama gona chintako
lilimi yaku maba
ukalibe invapo ilila itambika
koma iwe ukalibe itambapo
nankala chete nikunva ma rapper
azicha ati ndi nfumu
ntawizambili ndima yasa ndimi sala
koma ndi kunyu
azikazi amani konka alufuna celebrate perfume
so ntawi zonse ukandi ona am getting heads ngati nd*nkonyo
eeh nvani utenga mungelekezi amaba nyenga
ndilepela kukulupilila kuti ta brower ngati lupenga
east changu bwelani k*mweko
penyani ufulu tatenga
awa ma rapper amanveka same
sindiwa pala ngati nchenga
mwala pansi pamadzi
sukuda nkawa nanvula
am all about the green
ngati wachi ngono akashula pwee kata green
pepani ngati nalakwa
zina ndine nyopole
aya ma rapper ma broko amachita nga ni nkombole
[chorus ]
ma rapper, ana owa ngati afisi
yai samafika pa fupi
ngati upalauka upanga makwacha
anthu amati ndi nfiti, ndi nfiti
mponda matiki ndi mfwiti
nfumu, yai samazicha zicha nfumu
anthu ndiye amamucha nfumu
ngati wee kena kazi ndiwe nfumu
[verse 2]
imwe anyamata muli battery low ndine nili in charge
mukalibe kuleta beef choyamba train ngati ndingangi
funso flaffy kodi unga gwebane nababuni
awosheni nka wood like mufilika potema nkuni
kukana chakudya nk*meka
beef ifanika table
nyama ya rapper ni nyama yapwa
sk!lls nipasile chezo
wooked ngati ndi mbezo, wooked ngati ndi mbezo
wenyo nkali kupema ngakale chete alimaso
kunya kwa mpezeze k*mafunika pepala pafupi
kodi nchani mwabwelo kapa mkango kopanda nfuti
kupa ma rapper muchakwanu mulayesa nchafupi
alumbwana napapata don’t test me ngati ndi cooky
ufumu ndatenga ndine king ndakala ndine
down to earth ngati chitsime
mulimi saopa ndine
underground ngati kanfine
getting heads ngati vikuti
apongo pepani kuleta nsalamu mu dish
[chorus ]
ma rapper, ana owa ngati afisi
yai samafika pa fupi
ngati upalauka upanga makwacha
anthu amati ndi nfiti, ndi nfiti
mponda matiki ndi mfwiti
nfumu, yai samazicha zicha nfumu
anthu ndiye amamucha nfumu
ngati wee kena kazi ndiwe nfumu
[verse 3]
ngazi kaleza chikonda moyo sichikonda kopanda fanta
umoyo ungakale bwanji kopanda bamba
ndima konda achikazi aliko nasty ngati ndi nk*mba
chizungu chamati money talks
tumba lako inamanta
alu bwetu ndili chete ngat mwana atenga puuu
nili ngati nyankupiti ngona m’maba ntamanga dzulo
so dika beula ngati mazembe
ufanika uzibe it’s going down so mubwele naka mbwili
am too mokomoko ngati ofunta awili
chikwela ndiye chif*kwa chake mumagwa
me i have gat a new track ngati fuso latest
am sick mhmhm
[chorus]
ma rapper, ana owa ngati afisi
yai samafika pa fupi
ngati upalauka upanga makwacha
anthu amati ndi nfiti, ndi nfiti
mponda matiki ndi mfwiti
nfumu, yai samazicha zicha nfumu
anthu ndiye amamucha nfumu
ngati wee kena kazi ndiwe nfumu
yai samafika pa fupi
ngati upalauka upanga makwacha
anthu amati ndi nfiti, ndi nfiti
mponda matiki ndi mfwiti
nfumu, yai samazicha zicha nfumu
anthu ndiye amamucha nfumu
ngati wee kena kazi ndiwe nfumu
Random Song Lyrics :
- new room sm volume 1 congratulations - ostan stars lyrics
- jibber jabber 4 - zoan lyrics
- praying for love - elias sahlin lyrics
- spend one night - key! lyrics
- cold - just breathe lyrics
- not much (life is probably my girlfriend.) - don mastro lyrics
- please say goodbye - paper skies & aaron shirk & ehallz lyrics
- the show must go on (who's sorry now? it's never too late) - pink floyd lyrics
- ziploc - dizzy wright & demrick lyrics
- too young (traduction française) - louis tomlinson lyrics