lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

hear me - the very best lyrics

Loading...

chichewa
siyani dumbo
siyani umbombo
tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?
siya umbanda
siya zauchigawenga
kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?
siyani dumbo

hear me now
hear me now
hear me now
hear me now
hear me now
hear me now

siya kaduka
siya zokonda kuba
siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo
siyani kugona
siya kugona tulo
kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?
siya kaduka

hear me now
hear me now
hear me now
hear me now
hear me now
hear me now

dzaka mak-mi asanu
zatha kufika lero
mpaka lero umphawi
ukungophabe dziko
dzaka mak-mi asanu
zatha kufika lero
mpaka lero umphawi
ukungophabe dziko

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...