kadigong - sho madjozi lyrics
Loading...
*lyrics from snippet*
[chorus]
mayaz mayaz mayaz
gwira malaya nane ndilowe basi
mayazi mayazi mayazi
nkhani yamanyado olive mkhala pakati
mayazi mayazi mayazi
kuyilowa ndi mutu mopanda manyazi
mayazi mayazi mayazi
okudya ndalama samachecker balance
vina,tchola,tsika kadigong
kadi kadigong
kadi kadigong
[verse]
zinali plan kuti ndikukonde
wotsekemera ngati ndiwe chombe[?]
wotsekeleza ma guy onse, odi ndikapote
tizithire tikhale pa easy
ndili ndi mandede ngati ian lizzy
ndimakonda njonda zachimidzi[?]
akhale wa ulemu mfana wa peace[?]
Random Song Lyrics :
- loves me like a rock - the wailin' jennys lyrics
- mexican bus - floater lyrics
- just another guy (vocal version) - peter green lyrics
- дворы (yards) - зараза (zaraza) (xacvsquad) lyrics
- aeroplanino di carta - vacca lyrics
- one way out - sonny boy williamson ii lyrics
- till julia - cornelis vreeswijk lyrics
- memória - josé mauro lyrics
- many handle - chief keef lyrics
- gringo - cixi lyrics