lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

pogona - sevenomore (mw) lyrics

Loading...

[intro]
yah
oh*yah*yah
oh*yah*yah
oh*yah*yah
oh*yah*yah

[chorus]
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[verse]
k*mbali amandikana, amati ine ndine hule
k*mbali amandinyoza, ati ndine osauka
k*mbali amandikana, amangoti ndine mzake
k*mbali amandinyoza, ati ndimankakamila
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ine ndakusowa”
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ndili nawe nkhani”
komatu sakamba ayi, amangokhala pa easy
komatu sa*talker ayi, ndimangodziwa ma pg
ndimalakalaka nditabweza chipongwe koma ine zimandikanika
ndimalakalaka nditabweza choyipa koma ine zimandikanika
ndimamukonda ine, sindifuna atandisiya
ndimamufila ine, sindifuna ntamusiya
[chorus]
komabe, amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[outro]
yah*yah, yah*yah
yah*yah, yah*yah
yah*yah, yah*yah
yah*yah, yah*yah, prr

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...