palowa njoka - sevenomore (mw) lyrics
[pre*chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz*n*li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka
[verse 1]
amakufuna zikakhalatu zawavuta (yah, yah, yah, yah)
yah, amakufuna zikakhalatu zawathina (yah)
yah, koma ku party umva asabwere amene aja ndachamba
koma ku ukwati umva asabwere amene aja ndamowa (oh my god)
[pre*chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz*n*li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka
[verse 2]
yah, amafuna uzivutika
amafuna uzingopempha
amafuna uzisawuka
inenso ndekha ndisamapushe, yah, yah
pano p*n*lowa njoka
ka banja kajaso kanatha, p*n*lowa njoka (palowa njoka)
[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka
[outro]
yah, yah, yah, yah, yah
yah, yah, yah, yah, yah
panopa p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
panopa p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
p*n*lowa njoka
panopa p*n*lowa njoka, rr
yah, yachina seven adah
Random Song Lyrics :
- põe a mão na cabecinha - victor rodrigues lyrics
- show w... - wac toja lyrics
- bad news - omvr lyrics
- frisch aus der hose - sylabil spill lyrics
- king kong / observeer - kempi lyrics
- mtv rapfix acapella freestyle 2013 - rittz lyrics
- who we are (feat. miss palmer) - tom swoon lyrics
- a fan - drakeo the ruler lyrics
- dark side taking over - nonelikejoshua lyrics
- hnscc - the 1975 lyrics