awida - sagres 014 lyrics
#intro [joskido]
dzina langa ndine bunda kulanga ana chipwete chalunda
kugawa chibhalo zibhalo year0 k*musiya paukapolo
kanyokhe kanyokhe komabe end ndidzakuyenda
simud*nkula afana mukule kaye mukali khanda chuh
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd*nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd*nkati ndidzad*nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd*nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd*nkati ndidzad*nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#verse 1 [sagres 014]
nditangobwera k*mene ndima leader life ya hiphop
mfana wa ding mfana wa llz wosemphsna nditi zikwapu
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
mid am on zеro end i don’t know apa asabula
mix chimfana cha llz nd*nkangodzimva u bnd
kudzuka mammawa kuvaya pa commoz pena kugona ku gmt
#cont….[temano]
yama badman eeh, portal kuopsa ngati ndе ndiku vatican eeh
acting very bad pa bunda ndine veteran, shaa!!!
mutu wakula kugoba frus but still on a front line yeah
feeling vibes mix nde timango dripper aise
anyani anyani nkati bola mpeze pap
reaching my goals
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd*nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd*nkati ndidzad*nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd*nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd*nkati ndidzad*nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#outro
awida
awida
awida, onse achina ida awida
onse omwa ma ryder ma cider awida
Random Song Lyrics :
- nanx3 - van elie lyrics
- stand for summtin - sheek louch lyrics
- overreacting - olivver the kid lyrics
- summer dream - elris lyrics
- рай (paradise) - дима билан (dima bilan) lyrics
- every day is valentine's day - jan terri lyrics
- a storm of pouring rain washes away his name - jory canfield lyrics
- cant be stopped - lil insane brain lyrics
- moving on - blake bollman lyrics
- back of the line - crucifix lyrics