![lirikcinta.com](https://www.lirikcinta.com/statik/logonew.png)
sizokakamiza - sagonjah & tadala lyrics
Loading...
[hook: sagonjah]
sizokakamiza, chilungamo chimamasula
sizokakamiza, chilungamo chimamasula
[verse 2: tadala]
ati mnafela dzina, tada
bola nkafele zina, mama
msatelo mtima kutsina
mukafumula nkhuni taphikazi kupima
fupa lokakamiza,mphika nde ndiomwewu
izi zosakaniza,tizafumbwisa mbewu
k*mangozisempha, tikungosemphana
ndimangozileka lero tikungolekana
madzi saoleka,lero zaoneka
za pendapenda chilungamo chikasoweka
sizinga worke nanga daily waboweka
lilime ndi mpeni pano lako linanoleka
izi wakamba zija wapanga
ndikafunsa ichi iwe wagwanda
ndingoona ngati mfundo wamanga
ndikuchedwesa n’dakayenda mwali thamanga
Random Song Lyrics :
- safe - the house of love lyrics
- never cross them - plies lyrics
- rapsincorte vi - foyone lyrics
- my apologies - test-igo lyrics
- tangerine - aaron rizzo lyrics
- lovely - sal houdini lyrics
- how many liccs - teecee4800 lyrics
- the bidness - krizz kaliko lyrics
- kipele kiese - ferre gola lyrics
- особенная (special) - abdr. lyrics