lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mankhwala - sagonjah & tadala lyrics

Loading...

[intro: tadala]
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away
one spliff a day keep the evil away

[verse 1: tadala]
yolimidwa pa nyasa
golide weniweni no mizaza
mutu ukapweteka ndikuyasa
pepa neighbor ngati zimakunyasa
inditenge,indisiye ndili duuu kucheteka
pena kuseka ngati mtima suukupweteka
mankhwala
kuzitemela mumabala ndikakhala
ndayenela kudwala ndikasala
mitengo kuokela ngati m’malambe
iyi ndizadya mpaka ndizakalambe
ubwino wake kwa inu sarngakambe
a police ndi abale sangalande
kwani
imeneyo mma newspaper nde nkhani
ku mtundako akuba koma lekani
anangozazana anamaselempwani
how do you even tell this to a lame man?
[chorus: sagonjah and tadala]
eh ndikuyasa
moto,sindikuzima toto,kwanilitsa maloto
kwathu ndikunyasa
opeleka misonkho,onse olima mogo,angotsala ndi khokho
zinthu zanyasa
taona katangale, mzimu wa matafale, lira mayi wawaye
iwe dzuka nyasa
zitsotso zitsatse,pa msika zitsatse,tsamba lobiliwira liyase

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...