sitigawana - rudimental & the martinez brothers lyrics
[verse]
a phiri anabwela kuchoka ku harare eeh
a phiri anabwela kuchoka ku harare eeh
koma nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
ndati nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
a phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
makolo anga onse anamwalira ku dara
a phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
makolo anga onse anamwalira ku dara
[pre-chorus]
koma nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
ndati nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
a phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
makolo anga onse anamwalira ku dara
anamwalira ku dara
oh, sitigawana
[chorus]
oh, sitigawana
sitigawana
oh, sitigawana zida
umandikondera m’mene umandikondera ife
sitigawana zida
sitigawana
sitigawana zida
sitigawana
ife sitigawana, sitigawana
oh, sitigawana zida
sitigawana
sitigawana
oh, sitigawana zida
umandikondera
m’mene umandikondera
ife sitigawana zida
sitigawana
sitigawana
oh, sitigawana zida
umandikondera m’mene umandikondera
anamwalira ku dara
[outro]
koma nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
ndati nkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
a phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
makolo anga onse anamwalira ku dara
a phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
makolo anga onse anamwalira ku dara
Random Song Lyrics :
- strung up high - lord gabe lyrics
- hangod hallom - mangorise lyrics
- otázka času - ektor lyrics
- garde les yeux ouverts - busta flex lyrics
- ошибка (error) - egor muf lyrics
- gold digger - saucy santana lyrics
- i'm in the ghetto (north waves remix) - koma (koma) lyrics
- loversnight - supermax lyrics
- crazy talk - g.e.m.s (rapper) lyrics
- страна кошмаров (the land of nightmares) - devente's avenue lyrics