mubwere - ritaa lyrics
ritaa mubwere lyrics
oh, sispence, oh oh oh
ritaa.. h*llo?
(verse 1)
munachoka kuti mukukasaka ndalama
mpaka lero simunabwelerenso
munachoka kutisiya ndi amai athu
koma simunabwelere..
simumatumizanso chithandizo kunyumba
koma zoti mukuchita bwino tik*mva
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik*mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba..
(verse 2)
tinakula, otilera *n*li mai athu
kuvutika pamodzi ndi amai athu
komanso mutangopita
achimwene anatisiya
ana anu akungolira
chilichonse kuvutikira
phone yokha mukanatiimbira (h*llo?)
kalata yokha mukanatilembera (you know)
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik*mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
(bridge)
ohh, mubwelere kunyumba
oh, oh , oh ..
mubwelere kunyumba
(chorus)
Random Song Lyrics :
- cadê o vaso - débora oliveira lyrics
- driveway - fitz leland lyrics
- chirality - jt machinima lyrics
- chaka - algiers lyrics
- un amore anonimo - patrizia caselli lyrics
- peace and quiet - lew lyrics
- middle school! - tekyume lyrics
- cerebro de tivol - al2 el aldeano lyrics
- ptsd - dawin lyrics
- cheap fake - loverswasteland lyrics