ndiwe number one - revolver lyrics
[chorus-sir patricks]
chikondi ndichophweka ukapeza soul mate
uzakhala wokoma moyo wako wonse
ukazapeza namwali wachikondi ngati w-ngadi
ngati w-ngadi yeah
ndiwe number one (poti sukudziwa)
ndiwe number one (uleke kulota)
ndiwe number one (poti sukudziwa)
ndiwe number one ndimawelengela
[verse 1-revolver]
one, ndiwe one ngati mata
okuposa palibe iwe, ata
olo zinthu zitavuta bwanji ndikakhala ndiwe m’mtima mumakhala bata
two, ena kutokota timagontha nkhutu
its just us two
zima looks tho
siwe nkhw-ngwa, no
koma umandiwazatu
dont you ever forget
you all that i need, no meth
nthawi zonse dzina langa limakhala mkamwa mwa anthu ngati colgate
nd-nkakhala ndi uyu lero mawa ndi wina
but you is a keeper ngati pepe reina
this feeling is new to me
tabwela ndikuwuze what you do to me
(back to chorus)
[verse 2-revolver]
you blow me away you the bomb bae
uli hot ngati phwanya yaku bombay
i can look in those eyes all day
game ndimaisata but i dont play
ndinali player koma pano ndinabinya ah
wofuna kulanda zimudinya ah
mwini wake wa mtima w-nga iwe
umawala mu mdima w-nga iwe
you see i dont love you coz i need you, i need you coz i love you
olo nditaluza chili chonse i can still get through it as long as i have you
my love aint blind
imawona but it just dont mind
eh ili sisewelo
iwe wekha nzakuveka velo
(back to chorus 2x)
Random Song Lyrics :
- if i don't marry molly i'll die - justin hiltner lyrics
- christmas presents - murphdirt lyrics
- olvidar - zona ganjah lyrics
- was war der grund? - basstard lyrics
- yin yang - dosseh lyrics
- my world - d-tin lyrics
- jessli dovolíte... - prago union lyrics
- you've got the kind of nerve i like - tiny ruins lyrics
- musica romantica - banda la tunera lyrics
- nowhere else to go - wait for the day lyrics