angozo - piksy feat tay grin & lulu lyrics
chorus
angozo
safuna zoyambana angozo
angozo
safuna zokangana angozo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ndi ntondo ntondo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ntondo
piksy
wodya zake alibe mulandu
ali ndi tsoka wopanga za anthu
zawo zikuyenda
nsanje ndi matenda
zawo amanena ndi anthu angozo ndi ofewa
angozo sadzatheka
humble, selfless
sathoka za udolo wawo,
ndi katundu, amfumu
koma mmudzimu akulemera ndani?
(ndi angozo)
akazi abwino amagomera ndani?
(angozo)
pakati pawo alibe stress ndani?
(ndi angozo)
ndekuti awa angochedwa kupanga ziphokoso
i am the definition of angozo
chikhala nyerere you know bwenzi ndiri mdzodzo
tsono dzimakomo kutseguka
chikho chawo kusef-ka
zowapinga kupatuka
ineyo ndi angozo
chorus
angozo
safuna zoyambana angozo
angozo
safuna zokangana angozo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ndi ntondo ntondo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ntondo
tay grin
angozo mdi bad man
wa pa easy koma otchuka ngati gangnam
ndi ma chick amahita ngati van dame
sadzipopa ngati bubble gum
mfana ozitsata (ingofunsafunsa akuuza)
mfana ozisanja (ona motor akuphusha)
mfana wa chikoka (anthu onse mmudzi amamdziwa)
angozo!
olo mafana amatchula dzina
amakwana, amathina
anthu amadziwa ndi makina
mitu yawo imayima
angozo ndi head-cleaner
dziko limavina
apapa china nchina
ngakhale amene sakufuna apange salute
angozo!
chorus
angozo
safuna zoyambana angozo
angozo
safuna zokangana angozo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ndi ntondo ntondo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ntondo
lulu
angozo mmudzi nkhani ndi yawo
kulima minda opanda mvula kukolola
angozo mudzi ukamba za iwo
mulungu -n-lemba angozo ngokolola
ngakhale tsiku la ma dyelero
azimayi amangofuna angozo ayimbe ng’oma
ena akuti ng’omanso ayi
angozo tiwafuna pafupi ativinitse
kuntero ngozo ng’oma kuti booo
(ngozo ayimbe ng’oma oh oh)
kuntero ngozo stepe kuti seee
(ngozo ayimbe ng’oma oh oh)
kuntero ngozo ng’oma kuti booo
(ngozo ayimbe ng’oma oh oh)
kuntero ngozo stepe kuti seee
(ngozo ayimbe ng’oma oh oh)
angozo amuna anzawo nsanje
angozo modzichepetsa kuseka
angozo sangamalize chitelera
kuopa kuwadikira pa njira
chorus
angozo
safuna zoyambana angozo
angozo
safuna zokangana angozo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ndi ntondo ntondo
angozo angozo angozo
ndi ntondo ntondo
Random Song Lyrics :
- i forgive it all - mudcrutch lyrics
- grace alek naomi - le1f lyrics
- cold ice - dawgg lyrics
- tak wiele - kiszło brt lyrics
- okalma love - stos namou lyrics
- malo drugačije - arafat lyrics
- khodeti - sina hejazi lyrics
- armado em rossi - wet bed gang lyrics
- no wrongs - q boy chuck lyrics
- you'll lose a good thing - mcalmont & butler lyrics