uncondition-aleh - oti$ dean lyrics
[verse 1]
pali kenakake ka gel
kamaipasa moto sindimamva mphepo
ndipo kamandifika peni peni
peng ting mwanakazi ndika ngelo
ndine n0body
but she don’t even care ndine n0body
she believes one day i’ll be a somebody
ati maybe one day we’ll start a family
[pre*chorus]
ndika fine girl yeah kamandiwaza
lelo kabhowe, mawa kubhebhetsa
sangamvetsetse why timakondana
why, why
zikati zivute pena timakangana
mpakana 3 days osayankhulitsana
sangandisiye poti timamvana
(why why) timamvana
[chorus]
unconditionale amandikonda, amandikondabe
unconditionale amandikonda, amandikondabe
unconditionale amandikonda, amandikondabe
unconditionale amandikonda, amandikondabe
why why why why
amandikonda, amandikondabe
eh eh eh eh
amandikonda, amandikondabe
why why why why
amandikonda, amandikondabe
eh eh eh eh
amandikonda, amandikondabe
[verse 2]
koma uyu w*nga baby
sometimes amashupha zenizeni
samafuna ndizicheza nda achina jenni
ndizingopanga za iyeyo basi daily, daily
money, money, money, kfc
ku show amafuna kupita vip
ndikamwana kak*mpanda ka zi energy
she got a lotta love energy
[pre*chorus]
yeah kamandiwaza
lelo kabhowe, mawa kubhebhetsa
sangamvetsetse why timakondana
why, why
zikati zivute pena timakangana
mpakana 3 days osayankhulitsana
sangandisiye poti timamvana
(why why) timamvana
[chorus]
unconditionale nane ndimamukonda, ndimamukondabe
unconditionale ndimamukonda, ndimamukondabe
unconditionale ndimamukonda, ndimamukondabe
nane ndimamukonda, ndimamukondabe
why why why why
amandikonda, amandikondabe
eh eh eh eh
nane ndimamukonda, ndimamukondabe
why why why why
amandikonda, amandikondabe
eh eh eh eh
nane ndimamukonda, ndimamukondabe
[outro]
amandi*amandi*amandikonda
amandikonda
amandi*amandi*amandikondabe
amandi*amandi*amandikonda
amandikonda
amandi*amandi*amandikondabe
Random Song Lyrics :
- ttm - stixz lyrics
- duelo criollo - edmundo rivero lyrics
- schneeflocken - coodiny lyrics
- staple pants - cartier hendrix lyrics
- só falta você (cover) - ingrid solano & kayky freitas lyrics
- macariolita - claudio villa lyrics
- nightshow - sett osan! lyrics
- don't breathe (prod.capsctrl) - karmatheripper lyrics
- pray - bruntj lyrics
- better man - yung kronik lyrics