lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

iwe ndi ine - oti$ dean iii lyrics

Loading...

[verse 1: oti$ dean iii]
ukasekelera, ukamwetulira
ine thupi lonse nthumazi
sindikufuna wachikondi wina
koma iweyo basi
ukangodiyandikira
ine zonse kayale
ukangondinong’oneza
nzelu zonse balala
chif-kwa cha iwe

[pre-chorus: oti$ dean iii]
sinditha k-mvetsa
sinditha k-mvetsa
kodi zinakhala bwanji
lelo ndamupeza
lelo ndamupeza
w-nga w-nga wachikondi
muntima ndimanyadira
chif-kwa cha iwe
umandikwanira
pa iwe ndinathera

[chorus: oti$ dean iii]
ulibe compet-tion-ih
wawina kale
chikondi chopanda season-ih
ndichomwe tilinacho ife
ooh-oh x4
iwe ndi ine mpaka kalekale
ooh-oh x4
iwe ndi ine sitingasiyane

[verse 2: jyc9 jr]
chikondi chokoma ngati candy
palibenso wina angalande
palibenso wina angamake
iwe ndi ine nde mpaka kalekale
ndaima pachulu aliyense adziwe
mwaiwe ndapeza chikondi chamuyaya
sitizalekana baby sindizakutaya
ntima w-nga wakana kukonda wina

[pre-chorus: oti$ dean iii]
sinditha k-mvetsa
sinditha k-mvetsa
kodi zinakhala bwanji
lelo ndamupeza
lelo ndamupeza
w-nga w-nga wachikondi
muntima ndimanyadira
chif-kwa cha iwe
umandikwanira
pa iwe ndinathera

[chorus: oti$ dean iii]
ulibe compet-tion-ih
wawina kale
chikondi chopanda season-ih
ndichomwe tilinacho ife
ooh-oh x4
iwe ndi ine mpaka kalekale
ooh-oh x4
iwe ndi ine sitingasiyane

[brigde: oti$ dean iii]
iweyo ndi ineyo
paliponse kuyenda shosholo
iweyo ndiwe mg1
usamakaikire
moyowu siungatheke
kukhala opanda iwe

[chorus: oti$ dean iii]
ulibe compet-tion-ih
(eeeeeeeeeeeh)
wawina kale
chikondi chopanda season-ih
(chopanda season-ih-ih-ih-iiih)
ndichomwe tilinacho ife
(tilinacho ife)
ooh-oh x4
iwe ndi ine mpaka kalekale
ooh-oh x4
iwe ndi ine sitingasiyane

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...