lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kumpeta milombe - mufrika lyrics

Loading...

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh

ku mpeta milombe
kwathela alumbwana

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh

ku mpeta milombe
kwathela alumbwana

kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza

koma potsilizira pake eeh!

tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh

ku mpeta milombe
kwasila alumbwana

iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh

ku mpeta milombe
kwathela alumbwana

ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...