lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mtendere - molto zambia lyrics

Loading...

eastern power!

[pre*chorus]

kodi mu adziwa amfumu anu?
(do you know your chief?)
kodi mudziwa komwe muchokera?
(do you know your roots?)
ngati muna badwa akapolo
(if you are born a slave)
kodi mu udziwa mtendere?
(how do you know freedom?) x2

[chorus]

kodi mu’dziwa.. mtendere, mtendere, mtendere
(do you know.. freedom, freedom, freedom) x4

[molto verse 1]

chimandi wawa ndi kaona anthu osoba kuchuluka
timati bvuto ndi ana mwina ndi akulu ka!
ma bvalidwe osayenera kusamva kwa chuluka
a dube anati “back to my roots” iwe k*mbuka
ana auzyeni za kwao amveleko tu!
ayende k*mudzi kwao aoneko tu!
they learn about their ways aciteko do!
aoneko nyau nu bvina ngoma zili du*du!
khalani guardian angelo mutetezi
aphunzitseni zakwao ana a to z
they learn about dos and don’ts ndi cite izi
asa kule m’sinkhu tyala bembelezi
sungani nwambo musataye mdambo
dziwani cilankhulo chanu bambo
know more about your heritage nwambo
mhuuu! “miyambo”
[pre*chorus]

kodi mu adziwa amfumu anu?
(do you know your chief?)
kodi mudziwa komwe muchokera?
(do you know your roots?)
ngati muna badwa akapolo
(if you are born a slave)
kodi mu udziwa mtendere?
(how do you know freedom?) x2

[chorus]

kodi mu’dziwa.. mtendere, mtendere, mtendere
(do you know.. freedom, freedom, freedom) x4

[molto verse 2]

anati know where you are from
udziwe tsogolo lako
appreciate your mother tongue
udziwe lokolo lako
zitseko zonse zina sinkha
uza kh0m*lolako
minda zinasiya makolo
nawe kololako
ndine mwana m’ngoni osani sobeletsa
ndingo bvina ingoma osani konkeleza
ibangule mkango sinjenjemetsa
kalindula nje! no doc shebeleza
mtunda wama ola uyamba ndi tente eii!
are you actually free or mwina ndi nthete eii!
tsiku uzapita k*malo ali chete eii!
akakonsha za we suzakhala chete eii!
can you become so passionate about your roots, about your fruits, about your chiefs, kings and queens and let it dominate
you can never know where you are going nga sudziwa where you from
conde ndili ndi konsho eyy!
[pre*chorus]

kodi mu adziwa amfumu anu?
(do you know your chief?)
kodi mudziwa komwe muchokera?
(do you know your roots?)
ngati muna badwa akapolo
(if you are born a slave)
kodi mu udziwa mtendere?
(how do you know freedom?) x2

kodi mu udziwa..?
(do you know..?)

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...