lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

konkuno - mistah yemie lyrics

Loading...

[intro]
yeah yeah
yeah eeeh

yeah yeah

[verse 1]
seh uk*mandizembera
k*mayesa sinzazindikira
k*matchukisa m’maku limbira
kuti uyende ndine m’maku lipira
yeayii
koma zomwe ukupanga
mtima w*nga uk*maswa yeah
vuto ndi ine mwina nkana imakaye
nkhani nk*mava nk*maziika pa easy
lero ndabwera ndikufuna ndikuuze

palibe chisisi padziko lapasi
zina ndi izizi ndaziona basi
paja chokwawa chimak*mana nchozemba
olo utatani sunganamize onsewa

[pre hook]
dziwa ndik*manva aaa
mwina sukudziwa ndik*maona aaa

yeah yeah
yeah eee

[hook]
ndili m’mudzi momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndilikonkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah eee
eeeeee
ndili momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndili konkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah yeah
yeah

[verse 2]
girl umazinamiza yeah
ukamakhara yeah
ukamabwera nk*mazandi sekelera yeah
nk*makandi jeda yeah
nk*mandinena yeah
nk*mandi tchula ndine munthu opepera yeah

ndimapilira
ndimazindikira
utha kuzasintha ndeno ndimadikilira
koma pali chimodzi chomwe sumazindikira
yeah
ndichimodzi chomwe sumazindikira

palibe chisisi padziko lapasi
zina ndi izizi ndaziona basi
paja chokwawa chimak*mana nchozemba
olo utatani sunganamize onsewa
[pre hook]
dziwa ndik*manva aaa
mwina sukudziwa ndik*maona aaa

yeah yeah
yeah eee

[hook]
ndili m’mudzi momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndilikonkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah eee
eeeeee

ndili momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndili konkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah yeah
yeah

[pre hook]
dziwa ndik*manva aaa
mwina sukudziwa ndik*maona aaa

yeah yeah
yeah eee

[hook]
ndili m’mudzi momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndilikonkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah eee
eeeeee

ndili momuno ooo
(momuno, momuno)
mwina sukudziwa ndili konkuno ooo
(konkuno, konkuno)

yeah yeah
yeah

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...