holy - mic mash lyrics
verse 1
you’re holy, zoti ndinu oyera anthuwa akuseka
kunamizana kuti gahena kulibe sakufuna kuti nkhosa akuse ka
holy he is
ndikamachimwa sakondwa ndi izi
ndili pa easy comfort zone my soul he ease
be holy for he is holy his glory like bob the spirit i marry (marley)
william his will i am i aim higher with the holy spirit
mc, call me malawian jin (gin) the spirit in my bars oyera ufa
opanda yesu iwe ufa
ndili mu champions league uefa
satana atalanda madalitso yesu ana maka
ndinapulumuka dzina langa ana marker
akamati mulungu kulibe mudziko anthu akunamaka
tikhale oyela osati ophoda
sizachibwana palibe za phada
mtima wakowo mupatse alora
make the word beautiful ngati aurora
hook- issabel m king
you are mighty (zamoyo zinayi)
you are wonderful ( zimalambila inu)
you deserve all the glory (you deserve the glory)
for you are graceful, graceful you’re merciful
you are mighty
the king of all creations we worship you
verse 2
zamoyo zina zimalambira (oyera oyera)
mfumu yamafumu kalonga wa mtendere (oyera oyera)
he is holy; holy yeah my god is holy
be holy he’s holy the beginning and the end mulungu sanachimweko
sakanabwela ngati munthu sanachimweko
pa dziko chibuku sanachimweko
zinatheka bwa? padziko iye osakhala mu uchimo (sin)
dziko kudana naye iye k-mva kukoma ngati ali mu uchimo (honey)
anamugonjetsa satana kufa nkuuka sinzukwa anapha uchimo
not a player anafela ine (fellaine) pa mtanda pa calvary
he gave us the beautiful minds, call it recovery
he died for you and i gee (ig) no instagram he is my memory
be holy for he is holy and godly he never shares his glory
(hook)
outro
oyera oyera-2
Random Song Lyrics :
- 4 am in amsterdam (reaching into my brain) - waymad-beatz lyrics
- severina xique-xique - forróçacana lyrics
- bretagnes - dan ar braz lyrics
- cut that out - oak house lyrics
- dreamer - the b.b. & q. band lyrics
- no answer - dan lewandowski lyrics
- više se ne bojim - goribor lyrics
- way up - deraj lyrics
- elaborate lives (reprise) - elton john lyrics
- party party - charli xcx lyrics