lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

andisamala - mic mash lyrics

Loading...

verse – mic mash
amadyetsa mbalame zosalima
amalimbitsa zonse zosakhwima
moyo waulele anandipatsa ambiri ma hour
ndilibe chif-kwa chodandaulaso za mawa
mavuto angalimbe, hakuna matata, i matter to my father andisamala
dziko lingandinyoze, sindichita mantha, i’m never alone// i’ll never worship other gods like aaron
sawelengela phulupulu zanga
zomwe ndimachita ndi anzanga
ngakhale ndimachimwa mbuye w-nga sanditaya
ine ndikamaphwa iye amandipopa ngati tire
(eeeeh eeeh) you gave me life i lift your name higher
(eeeh eeeh) you the reason why ndikuimba ndi choir
ndithange ufumu wanu zinthu zanu ndizakwaya
at the end of the day i don’t want to go to fire

hook – siggy kim
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala

verse 2- siggy kim
feeding feeding is what you do
you give food to the poor and the need
lord healing healing is what you do you heal all the people who are sick in beds
your the one who gives directions to them
your the one who wipes away all the tears
i will worship you
i will always praise your name
your the one who controls all the world

hook – siggy kim
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala
andisamala andisamala
andisamala amasamala adzasamala

mudzasamala baba
mudzasamala
mumasamala oooh ooooh
oooh oooouuh ooooh

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...