lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

sama - maurice 26 lyrics

Loading...

mmmh mmmm

maurice
ooooh sama!

ndisaname ndikudadwa ine nowadays ukukwiya
foni yanga unasiya kuyankha kapena mwina ndik*makubhowa
ngati pali chomwe ndidalakwa nanga bwanji osafotokodza
action sipeleka uthenga sindingadziwe chomwe chakuvuta
(my heart) i had sacrifices to you ndisaname (zik*mandiwopsa)
tell me what’d think if is over let me know

hook
samala
( samala wako)

chengeta a!
( chengeta wako)

zimayamba bwino x² za smart ngati namwino maonekedwe ngati w*ngwiro ooo o oh

chikondi chathu chikhale mbambande ansenje tiwaponye mzenje kotero sangatilekanise ( sangatilekanise)

amakulonjedza zoti sangathe cholinga mtima akuswere
amakondwa ukugwetsa msomzi i i i i!
hook 2

hook
samala
( samala wako)

chengeta a!
( chengeta wako)

sama o oh ee
(ooooh)

samala owoh
(o ei)

oh samala owoh
(samala!)

hook
samala
( samala wako)
(sa ma la )

chengeta a!
( chengeta wako)
(samala owoh)
hook
samala
( samala wako)
( samala)
chengeta a!
( chengeta wako)
(sa ma la)

hook
samala
( samala wako)
wako ndiwako)
chengeta a!
( chengeta wako)
(wako ndiwako)

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...