lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

je m'apelle - mario bro's (mw) lyrics

Loading...

[intro]
ayo landie
aseh trappy

[pre*chorus: crispy malawi]
umazimva money, kodi uli ndi chani iwe?
sindufuna ya liz koma tusaka mandede
umazimva ding dong koma uli mtandire
kundikoka kuti ufike level ya ine (level ya ine)
ine si size yako
ine si size yako
ine si, ine si, ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine siiii

[chorus: crispy malawi]
comment tu t’apelle, je m’apelle
comment tu t’apelle, je m’apelle spe
comment tu t’apеlle, je m’apellе
comment tu t’apelle, je m’apelle spe

[verse 1: ace dirty]
size kukana (size kukana) pena kuthina (pena kuthina)
eyes on the prize koma bola osatsizina
dreams of brighter days koma ndichoka midima
mulungu alinafe a malawi kukonda kukhwima (yea)
iwe si size yanga
chabwino ndizophweka nanga bwanji sumukupanga?
i just want the money now azanga ndipatseni zanga
ngini inayima koma bwanji sumukukankha?
mukuti muku baller nanga bwanji sumuku dunker?
[pre*chorus: crispy malawi]
umazimva money, kodi uli ndi chani iwe?
sindufuna ya liz koma tusaka mandede
umazimva ding dong koma uli mtandire
kundikoka kuti ufike level ya ine (level ya ine)
ine si size yako
ine si size yako
ine si, ine si, ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine siiii

[chorus: crispy malawi & lil al]
comment tu t’apelle, je m’apelle
comment tu t’apelle, je m’apelle spe
comment tu t’apelle, je m’apelle
comment tu t’apelle, je m’apelle spe (yea, yea)
(ayy, ayy, ayy)

[verse 2: lil al]
gimme me a minute, i’m tryna feel it
we gettin’ high sky’s the limit
vibe ili bho sikufunika remix
sindikamba mbwelera checker lyrics
gist ya mada inasiya kupenga[?]
still tryna be high ma guy akulenga[?]
everywhere every record tikubreaker[?]
cookin’ up zik*mveka ngati tik*mveka[?]
sindimadziwa kuti iye ndi kape
ndamukhulukira vuto ndi amake
sizundikhudza olo tidane ilakwe ilakwe
ndizidyabe money yeah

[pre*chorus: crispy malawi]
umazimva money, kodi uli ndi chani iwe?
sindufuna ya liz koma tusaka mandede
umazimva ding dong koma uli mtandire
kundikoka kuti ufike level ya ine (level ya ine)
ine si size yako
ine si size yako
ine si, ine si, ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine si size yako
ine siiii

[chorus: crispy malawi & lil al]
comment tu t’apelle, je m’apelle
comment tu t’apelle, je m’apelle spe
comment tu t’apelle, je m’apelle
comment tu t’apelle, je m’apelle spe

[verse 3 : 60 grams]
comment tu t’apelle, je m’apelle dripavelli (slatt)
chaka chino nde mukhawula zedi
nde mukamva kuwawa mukaphweketsa don’t regret it (ayi)
zopusa ine ayi turn my eye to [?]
fell in love with syrsup kuchotsa clangs now i’m faded
tungopusha dancehall ku lilongwe ndi achina dirty

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...