ofunika ku worker - malumbo kondowe lyrics
verse 1
ndikaona komwe ndachokera
zomwe amkanena masten zija ndizomveka
mwana w*nga moyo siophweka
kuti ulimbe pa town zimafuna ku worker
osagona, k*menya tima hustle kuwonesetsa kuti chilichonse chikutheka
osaiwala mulungu patsogolo
tsiku ndi tsiku 2 dzina lake kulikweza
yeah! you really have to strive hard
if you really wanna make it this far
don’t rely too much on people
otherwise you will get yourself stressed out
limbikila school mwana w*nga
tizibwana moyo mu tachepetsa
ndimafuna mzaone utapanga gala
kenako ukuyendela ka sienta
chorus
ofunika ku worker
ngini singathеke utangokhala pansi neba
ghetto yuthi don’t strеss yeah
ingolimbikila one day zizatheka ah ah
ofunika ku worker
if you really wanna make the paper
(if you really wanna get the paper)
ghetto yuthi don’t stress yeah
ingolimbikila one day zizatheka
verse 2
there’s no shortcut to success
mwana w*nga ukufunika ku worker basi
sizofuna mpaka kukhetsa mwazi eti
ndicholinga choti uzaiphule fast
nah! making money is a process
pena umapeza nthawi zina ayi
osamapangaso za corruption
akazak*manga bail yako adzapereke ndani?
yeah! ndikamakamba zo worker eti
sitikutathauzatu ku vepi kokha
huh! you can be doing ka business
make sure it’s clean
osati ya illegal one
now
let’s get into the scriptures
timve amati chani zokhuza ku worker eti
genesis 3 verse yake ya 19
go and read it mukamva kuti ikuti chani
Random Song Lyrics :
- mankurt - shaours lyrics
- horses - matthew dear lyrics
- pay your debts - r2jbros lyrics
- burb - billy lemos lyrics
- anshey ha'botz - אנשי הבוץ - hapil hakachol - הפיל הכחול lyrics
- paranoya - fery lyrics
- run me down - little charlie & the nightcats lyrics
- бэнji's (benji's) - may wave$ & ameriqa lyrics
- sunberry gate - kleenex girl wonder lyrics
- down in vieux cannes - vira talisa lyrics