chifundo nane - lawi lyrics
[intro]
ayy
chifundo nane
chifundo nane
oh, chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
mtima w*nga don’t you worry
everything is gonna be alright
[chorus]
ambuye ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
mtima w*nga sudera nkhawa
chif*kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w*nga sudera nkhawa (oh no)
chif*kwa ali ndi chifundo nane
[verse 1]
machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
mutazindikira zamumtima mw*nga mukhoza k*mandisala
m*th* kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m’ndende
ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
ndiye amene anandipanga amandidziwa
zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
amatsegura manja ake ndi kundik*mbatira
[chorus]
oh, ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nanе
mtima w*nga sudera nkhawa
chif*kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w*nga sudera nkhawa (oh no)
chif*kwa ali ndi chifundo nanе (oh, yeah)
[verse 2]
ayi*yayi*yayi
ayi, ndachoka kutali, moyo w*nga ndi umboni
wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
pomwe adani anga andik*mbira mitsinje
wandimangira mlatho, ndayenda powuma
wandifewetsera zolimba zanga
[chorus]
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ine mtima w*nga (sudera nkhawa chif*kwa ali ndi chifundo nane)
ine mtima w*nga (sudera nkhawa
chif*kwa ali ndi chifundo nane)
Random Song Lyrics :
- pressure - cypaq lyrics
- o mundo tá girando - mentenativa lyrics
- béni - alkpote lyrics
- anger - the tiger lillies lyrics
- flieh von hier - adam angst lyrics
- villain. - unknxwn lyrics
- auf zum thron - miko lyrics
- roadless maze - xxxoriginalsinxxx lyrics
- west end (yea eh) - the sorority lyrics
- wuala - kolorofonia lyrics