lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

yendabe - kineo madness & aidfest madness lyrics

Loading...

[intro: kineo madness]
yeah
janostep[?]
alright

[chorus : aidfest & aidfest & kineo madness]
umati yendabe, yendabe
usatope usaf**ke (usaf**ke)
yendabe, yendabe
usatope, usaf**ke

[post*chorus: aidfest & kineo madness]
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako

[verse 1: kineo madness]
ndawona sindingakwanitse, mene akupangira azinzanga
awa *n*li [?] andidutsa pompaja
mavuto andikakamira, mwayi wanditalikira
komabe yendabe, yendabe
ukagwa uzidzutse uzistsatse
mavuto samatha mbale koma chilimikabe
kakamiza jah [?]
palibe chovuta pa town[?] kuyenda mpaka kukafika
[chorus : aidfest & aidfest & kineo madness]
umati yendabe, yendabe
usatope usaf**ke (usaf**ke)
yendabe, yendabe
usatope, usaf**ke

[post*chorus: aidfest & kineo madness]
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako

[verse 2: aidfest madness]
sindinali chonchi inе (ine), koma chif*kwa chamavuto ndimalimbika
and i don’t wanna go back to the old days
k*maziwa pano ndinaphunzira
za[?] sizilephеra koma ife timayendabe
olo katundu akulemera mavuto onse timasenzabe
nde iwe yenda, yenda
kholo ili ndiyawekha, wekha (eya)

[chorus : aidfest & aidfest & kineo madness]
umati yendabe, yendabe
usatope usaf**ke (usaf**ke)
yendabe, yendabe
usatope, usaf**ke
[post*chorus: aidfest & kineo madness]
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako
ukafika, ukafikako

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...