manjenje - kelvin sings (mw) lyrics
[intro]
mm, yeah, yah
[verse 1]
ukadzuka m’mamawa nkuyamika yehova (yehova, yah)
nk*mudalira kuti mavuto ako awasowa (awasova)
ebeneza, ndikutali wakuchotsa, yeah, yeah
pakamwa pako matamando osasosa, yah
[chorus]
amakuwopa awa, oh*no*no
amachita manjenje, oh*no*no, no*no, no*no
amakuwopa, awo, yeah, oh*no*no*no
amachita manje*, amanjenjemela nawe
[verse 2]
mavuto opanda kuwapempherera
ndyelekezi akawona zotelezi amasekelela, yeah
akondwera akawona kuti ku tchalitchi watenga tchuti, yeah
m’maganizo sungatsutsike m’mayesero akati alunjike
ukagwadwa ndikupemphera, k*midima k*matekeseka
ukamudziwa namalenga, ndizovuta kutekeseka
[pre*chorus]
poti nkhondo uk*menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda ndidziko nk*mayenda naye yawe
[chorus]
amakuwopa awa, no*no*no*no
amachita manjenje, oh*no*no*no*no
amakuwopa awo, oh*no, no*no, no*no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[verse 2]
poti kupempheraku ndi nkhondo (rethe)
adani satopa kuzinga mikondo
pambuyo payesuyo londo
you already know zikavuta ndimagwada pama*
kuyitanila conqueror
nchipululu simokhala
palibe chomulaka
azaveka adani juzi mu october, yeah
you’re royalty, vala chisoti chako
the rest is vanity, iwe izi sizako
[pre*chorus]
poti nkhondo uk*menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda nk*mayenda naye yawe
[chorus]
amakuwopa awa,yah , no*no*no*no
amachita manjenje, oh*no*no, no*no
amakuwopa, awo, oh*no, no*no, no*no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[bridge]
akazindikira what the almighty has inside of you
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
[chorus]
amakuwopa awa,yah , no*no*no*no
amachita manjenje, oh*no*no, no*no
amakuwopa, oh*no, no*no, no*no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[outro]
amakuwopa, awo (woo)
amachita manjenje (yeah)
amakuwopa awo
amachita manjenje, manjenjemela
Random Song Lyrics :
- way out - tiffany likoudis lyrics
- δεν αντεχω - skliros lyrics
- one - glvsshouse lyrics
- tænk på det, pt. 3 - mdmasger lyrics
- girl sittin' up in a tree - burl ives lyrics
- stereo earphone - ambr (jpn) lyrics
- yaşamaq lazım ("son arzum fahişə" filmindən) - noton lyrics
- meditation, pt. 3 - kieran the light lyrics
- 223 - vinshoodstar & ohstars9 & yung honey lyrics
- eu fico de boaça - thiago martins lyrics