mpendadzuwa - kay sadik lyrics
[verse 1]
lija ndikale nd-nkapanga zibwana
ndichikondi
poti tsuna yeni yeni yaine
yimasowa
eeya n’dakondapo ena wokongola
koma chikondi chawo nakhala mbola
n’dakondanso wosandikonda
wokonda chuma (wokonda chuma)
koma iwe chibwelele
moyo w-nga unasinthaa
ndati iwe chibwelele
nzeru zanga zinakhwimaa
[ hook ]
umandizula mtima
ukamwetuliraaa ukasekeleraaa
iwe
umaf–ketsa mphavu ya mdima
ndiwe chiphadzuwaaa
ndiwe mpendadzuwaa
iwe ndi nyenyezi
[ verse 2 ]
aliyense alinacho choyamikila inu
mulengiyo
ndiyamika pondipatsa iwe coz
having you is not a joke
ndiye ufusefuse ndi angati
iwe ufufuze ndi angati
wompeza wabwino wokhulupilika
ndiwowelengekaa
n’chif-kwa chake sindifuna
kukutaya iwee
ichi nchif-kwa chake sindifuna
kukunyoza iweeyoo
[ hook ]
umandizula mtima
ukamwetuliraaa ukasekeleraaa
iwe
umaf–ketsa mphavu ya mdima
ndiwe chiphadzuwaaa
ndiwe mpendadzuwaa
iwe ndi nyenyezi
[ bridge ]
iwe ukusiyana ndi enawaaa
iwe ukusiyana ndi enawaaaa
you’re so unique girl
your lifestyle (is) real and simple
you’re so unique girl
your lifestyle (is) real and simple
[ hook ]
umandizula mtima
ukamwetuliraaa ukasekeleraaa
iwe
umaf–ketsa mphavu ya mdima
ndiwe chiphadzuwaaa
ndiwe mpendadzuwaa
iwe ndi nyenyezi
Random Song Lyrics :
- wrong guy pt 2 - rah slz lyrics
- this house is haunted - atriarchy studios lyrics
- getrieben - hart to attack lyrics
- digital love - crimson red lyrics
- la mort - t2g lyrics
- four seasons - beny jr lyrics
- прикольный (cool) - last6last! lyrics
- treat your fuck - laputa lyrics
- money to make - reefuh lyrics
- erm what the sigma? (from the motion picture "rizzie") - jelly house lyrics