lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kwanu ndi kwanu - jeg tellem lyrics

Loading...

woyee yeah yeah
osamayiwala kwanu
tellem
osamayiwala

kwanu ndi kwanu mhuu
nthengo mudalaka njoka aaah
kwanu ndi kwanu mhuuu
nthengo mudalaka njoka aaah
kwanu ndi kwanu mmhu eh
ndi kwanube
kwanu ndi kwanu mhhu eh
ndi kwanube
kwanu ndi kwanu mmhu eh
ndi kwanube
nthengo mudalaka njoka aaah
penapake zikavuta iwe
ndikwanube
usamachite manyazi
ndikwanube
utha kubwerera konko
ndikwanube ah ah aaaaah

osayi wala
dzuwa likawala
yemwe anakubala
yemwe anakusamala
pamene ukudwala
usanakwela ladder
kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka
uzakufunabe olo utachoka
mukanyozela muzatenga matsoka
osalora azako aziku locker

kwanu ndi kwanu mmhu
nthengo mudalaka njoka aah
kwanu ndi kwanu mhuu
nthengo mudalaka njoka aaah

munachoka kunyumba kalekale mwati munatola ka joker
koma muzabwerabe kwanu nthеngo munalaka ka njoka
mwasintha maw*nga mwasintha khungu mapeto ake ndi matsoka
muzatipeza zinthu zikazavuta pano tingopеnya ndi maso
pa maliro simumapezeka
k*manda simumapezeka
koma kuti mugone pansi lero lomwe k*manda omwewo mupezeka
anapita kalekale kokawonekela eh
koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh
pena nk*mati njokayo mwina nthengo yasochela
koma azatipezabe mizimu sikukondwera
kwanu ndi kwanu mmhu
nthengo mudalaka njoka aah
kwanu ndi kwanu mhuu
nthengo mudalaka njoka aaah

yeah
galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji
uzigomela malawi kwanu kuno sungasowe mtaji
funsa neba amasililanji
mtendere umayambila chitipa kuthela ku nsanje
warm heart ku mpanje
uzingotakata mpakana uzatsegula maloko
kutukula dela lakwanu akhale ako maloto
kwanu usakuluzile hope
ukavaya abroad kusaka guap
tsiku lomwe uzafike pa top
kwanu uzakuyikeso pa map
mukanabwera
mwakhalitsa
anzanu ochenjela
goshen amangitsa
lemme explain
kulibeko malo ngati pa den
tufunika mindset change
osangokhalila kupanga complain
yeah yeah
kwanu ndi kwanu mhuu
nthengo mudalaka njoka aaah
kwanu ndi kwanu mhuuu
nthengo mudalaka njoka aaah
kwanu ndi kwanu mmhu eh
ndi kwanube
kwanu ndi kwanu mhhu eh
ndi kwanube
kwanu ndi kwanu mmhu eh
ndi kwanube
nthengo mudalaka njoka aaah

kamdothi iwe bwerera ku nyumba iwe
kamdothi iwe uthela moyenda iwe
kamdothi iwe aaaaaah
kamdothi iwe aaaaaah
kwanu ndi kwanu mfana
town ikasolobana
uk*mbuke padzana
bwerera kwa amama

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...