nilandileni - james sakala lyrics
chikondi iyee ×5
nalila eyy nazo zapaziko
nadandaula ine nazo zapaziko ba zanga nee
ndaba uyu umoyo naupuzila molimba
n′nakana waulesi kana kulibikila
koma lelo napeza chikondi chobambana eyy
sichiziweza yai chilibe sanje aye
chimapirira ichi nichikondi cha zoona
amalume nilandileni
nabwela n’dchikondi chobambana chapaziko
azanga nilandileni
nabwela n′dchikondi chobambana zapaziko zonse zintu(abale banga)
ichi ni chikondi chochokela kwa abuye yesu
(ooh abale banga aayy)
ichi nichikondi chochokela kwa abuye yesu
chikondi iyee×2
nalema nazo zotukanidwa kwa bale banga aye
nalema nazo zonozidwa kwa alongozi banga
kodi sumumaona chisanzo chinasiya abuye yesu
sitigalese kubonya ma party wabo
anadiya nao chimwa kubulumusa mbamba
kuchilisa aliyense opanda usanka
uyu ndiye mutima nimafuna kukala nao ooh…
mai kalanga neo
amalumbe nilandileni
nabwela n’dchikondi chobambana chapaziko
azanga nilandileni
nabwela n’dchikondi chobambana zapaziko
zonse zintu
ichi nichikondi chochokеla kwa abuye yesu
(ichi nichikondi)
ichi nichikondi chochokela kwa abuyе yesu×2
chikondi ×3
tiyeni tigilane manja
tiibenibo za chikondi×2
oooh…
ichi chikondi chachokela kwa abuye yesu×2
tiyeni tigilane manja
tiibenibo zachi nsaglalo…×2
ichi chikondi chochokela kwa abuye yesu×2
Random Song Lyrics :
- suicide & qancıq - vvsvaupra lyrics
- where i find hope - hornet's daughter lyrics
- my journey has begun - executed lyrics
- din - the western ghats lyrics
- money - wavy navy pooh lyrics
- wrath of steel - validor lyrics
- le rocher - daniel brossier lyrics
- 0 rischi nel love - mara sattei lyrics
- lost thoughts - austic lyrics
- so good to me - keb' mo' lyrics