lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

wandilonjeza - james chirwa lyrics

Loading...

[intro]
on it!…

[verse 1]

ndak*mana naye
mamuna wa mtanda
mfumu ya mafumu
kalonga wa mtendere

ndak*mana naye
mamuna wa mtanda
mfumu ya mafumu
kalonga wa mtendere

ali ndi chikondi
chake chopanda malire

ndiye amene mpaka kale
ine ndizakhulupilira

nthawi zonse
mtima w*ngawu ukondwera
naye
yeyeye
[chorus]

wandilonjeza
kuti sadzandisiya ndekha

wandilonjeza
kuti sadzalora mteleleke

wandilonjeza
kuti anditsogolera njira

wandilonjeza
kuti ine sidzasowa kanthu

[verse 2]

iye
ndiye nyali
mu njira yanga
(mu njira yanga)

iye
akudalitsa
ntchito za manja anga
(za manja anga)
ndikuyenda
mu chisomo chake
ndili nji! sindingagwedezeke
sadzandisiya ndionongekе
sidzasiya kutama dzina lake

ndiye amenе mpaka kale
ine ndizakhulupilira

nthawi zonse
mtima w*ngawu ukondwera
naye

[chorus]

wandilonjeza
kuti sadzandisiya ndekha

wandilonjeza
kuti sadzalora mteleleke

wandilonjeza
kuti anditsogolera njira

wandilonjeza
kuti ine sidzasowa kanthu
[bridge]

kuti sadzandisiya ndekha
(siya ndekha)

kuti sadzalora mteleleke
(mteleleke)

kuti anditsogolera njira
(lera njira)

kuti ine sidzasowa kanthu

[chorus]

wandilonjeza
kuti sadzandisiya ndekha

wandilonjeza
kuti sadzalora mteleleke

wandilonjeza
kuti anditsogolera njira

wandilonjeza
kuti ine sidzasowa kanthu

[outro]

wandilonjeza…

wandilonjeza…

wandilonjeza…

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...