lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

taona - james chirwa lyrics

Loading...

(verse 1)[james chirwa]

yeah…
on it!…

pano
kupemphera kuja
sikuku mandipatsa feel
ndimakhala busy
kulongosola zimadilu
zinthu zinasintha
always kuganiza zama bill
i got a lot of things to do
sindingakwereso hill

uthenga ndiwoti chaka
chino ndilemela
osati zina zija zijazi
zopanda mutu
nanga adzabweraso mpaka liti?
tingozitaya zingatipwetekese
mutu

makolo akundisayiza heavy
mwina sakuona bhobho
kuchigama
kuti nditha kuyendatu
mmene ndingathere
kwawo kunatha
anandiphuzitsa grammar
mtundu
wakwithu nikatundu mzito
imwe kufuma
vilije ntchito
bwenu ise tekha tekha
ngati dziko
m*th* kulowa joni
kayaso maputo

[chorus]

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa

taona
(ayeee!)

taona iwe
(ayeeeh!)

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa

taona
(ayeee!)
taona iwe
(ayeeeh!)
yeah!

(verse 2)[levison masamba]

mtengo wa mkuyu ukadzayamba
masamba
dziwa kuti nthaaawi ija
yafikaa
lero tako ko ko komedwaa
mpaka taso so so socheseretsedwa

chikondi ndiye chazilala
nyali za ambiri zazima
kwadza ziphunzitso zonyenga
ngati za nzeru ukamva
usamulole oyipa kukuphumitsa kolona
nthawi ndiyo yam*th*ra
injury time ikutha

[chorus]

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa
taona
(ayeee!)

taona iwe
(ayeeeh!)

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa

taona
(ayeee!)

taona iwe
(ayeeeh!)

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa

taona
(ayeee!)

taona iwe
(ayeeeh!)

ambuye anati!
nthawi yobwera ine siyidzasowa

taona
(ayeee!)

taona iwe
(ayeeeh!)
yeah

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...