lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

sindichoka - gwamba lyrics

Loading...

[intro: beracah]
(dj slay)
oh, yah, yah, yah

[verse 1: gwamba & beracah]
zambiri yanu ndinamva
akhungu onse, osamva
ena osayenda, kungowakhudza inu zawo zinayenda
nane ndifuna mundikhudze, chonde musandipitilire
ndatsegula manja, mulore mzimu wanu ukhazikike
yesu anamva mphavu zikuchoka
nzimayi wina wake atamugwira
mavuto ake onse ndikuchoka
amadwala basi iye ndikuchira
nane mbuye mundigunde
mukandiwolotse pamafunde
ndikudziwa pena ndine nkhutuk*mve koma mukafuna kukandi*user munde*useh

[chorus: beracah]
mukandikhudza, nyengo zanga zisintha
mukandikhudza, nyengo zanga
mumachita zazikulu yesu ndinamva (sinkayika konse)
i wanna see your glory, yeah, i wanna testify (ukulu wanu ndiwuwone)
koma sindichoka, choka, choka
mpaka mundikhudze, khudze, khudze
koma sindichoka, choka, choka
mpaka mundikhudze, khudze, yeah
[verse 2: gwamba]
mbuye w*nga chonde mundikhudze
ndikalakwitsa chondе mundiwuze
ndikamachapa chonde mundikhudze
osalola satana andizunzе
zolakwika zonse muzichotse
inu ndi amene mungakonze
pandekhapa palibe ndingachite nde chonde muzindisamalira nthawi zonse

[bridge: gwamba]
chonde musalole moyo w*nga, satana adzalepo zizanga
chonde musalole mbuye w*nga, satana kulowa in m’moyo

[chorus: beracah]
mukandikhudza, nyengo zanga zisintha
mukandikhudza, nyengo zanga
mumachita zazikulu yesu ndinamva (sinkayika konse)
i wanna see your glory, yeah, i wanna testify (ukulu wanu ndiwuwone)
koma sindichoka, choka, choka
mpaka mundikhudze, khudze, khudze
koma sindichoka, choka, choka
mpaka mundikhudze, khudze, yeah
mpaka mundikhudze ineyo
mpaka mundikhudze, yeah

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...