werenga - faith mussa lyrics
[verse 1 : faith mussa & madalitso band]
nane ndapambana chani? (ndapambana chani?)
abale ndapambana chani? (ndapambana chani?)
madalitso mukundipatsawa (ndapambana chani?)
mbuye madalitso onsewa(ndapambana chani?)
ambuye ndapambana chani?(ndapambana chani?)
[pre*chorus: faith mussa & madalitso band]
oh ndapambana chani? (ndapambana chani?)
madalitso mukundiwunjikira wo(ndapambana chani?)
ndikuchita kusowa kokatengera ine(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani ine?(ndapambana chani?)
ndapambana chani? ine ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
ine ndapambana chani? (ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
ine ndapambana chani?(ndapambana chani?)
inu madalitso onsewa(ndapambana chani?)
[chorus: faith mussa, madalitso band,faith mussa & madalitso band,]
werenga, werenga, werenga
werenga, werenga, werenga madalitso ako
oh madalitso ako (madalitso ako)
oh madalitso ako (madalitso ako)
werenga, werenga, werenga
werenga, werenga, werenga madalitso ako
oh madalitso ako (madalitso ako)
oh madalitso ako (madalitso ako)
[pre*chorus: faith mussa & madalitso band]
oh ndapambana chani? (ndapambana chani?)
ine ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
abale ndapambana chani? (ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
eh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
abale ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
abale ndapambana chani?(ndapambana chani?)
abale ndapambana chani?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani?(ndapambana chani?)
inе ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
ine ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
ine ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
oh ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
ine ndapambana chani ?(ndapambana chani?)
[chorus: faith mussa, madalitso band,faith mussa & madalitso band]
wеrenga, werenga, werenga
werenga, werenga, werenga madalitso ako
oh madalitso ako (madalitso ako)
oh madalitso ako (madalitso ako)
werenga, werenga, werenga
werenga, werenga, werenga madalitso ako
oh madalitso ako (madalitso ako)
oh madalitso ako (madalitso ako)
iwe madalitso ako
madalitso ako, madalitso ako
iwe madalitso ako
madalitso ako
Random Song Lyrics :
- booze city - solinger lyrics
- infinite love - ynkeumalice lyrics
- sick fuck - moving in silence lyrics
- none of my business - shazza lyrics
- that man - kourosh yaghmaei lyrics
- toy box - lubless lyrics
- over it - sephora_official lyrics
- hard - ploegendienst lyrics
- bare knuckle - mckinley dixon lyrics
- ân - kiliseler ve liseler lyrics