lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

ali dere - faith mussa lyrics

Loading...

[chorus]
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwotere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwothere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye

[refrain]
well try to know me better,before you talk about mе

[verse]
ali dere
nthawi zina umati ndine wabwino
nanga lеro bwanji ukuti ndine woyipa?
koma ine ndiwe sitinak*manepo?
koma ine ndiwe sitinachezepo?

[refrain]
well try to know me better,before you talk about me

[chorus]
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwotere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ali dere
ali dere uyuyu
ndiwotere uyuyu

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...