lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

theka - emmie deebo lyrics

Loading...

[intro]
roger, clock
ah aah aaah aaaaah
emmie again deebo ah

[verse 1]
unali pano dzulo crying
utatupa ndima fight
kukhala osagona all night, that’s alright
koma akangoti “hey hey”
kukhosi kwako kuti mbe mbe
umayiwala ndiwe ngenge
malangizo athu sumamvela

[pre*chorus]
dzulo wandiwuza kuti mwasiya k*mvana
watopa ndi khalidwe lake lachibwana
lelo ndakupeza uli naye pa foni
ukuti sungakwanitse kukhala alone yeah
umakopeka nzanga, umabalalika msanga
umakopeka nzanga

[chorus]
simuchedwa kugwa, simuchedwa kulola
m’makonda zachikunja
muposte pa status bola
akakutchula honey sweetie
(umakhala watheka) eh eh hee eh
akati tik*mana liti
(umakhala watheka) oooh oooh
[verse 2]
ndimuthu yemweyo, anakulonjeza zina
dzulo wampeza ndi wina
umati umusiyila pompo
you don’t mean it anyway
come a likkle likkle ting gets on your way
mumakomedwa inu
n’chif*kwa mumatoledwa inuyo

[pre*chorus]
dzulo wandiwuza kuti mwasiya k*mvana
watopa ndi khalidwe lakе lachibwana
lelo ndakupeza uli naye pa foni
ukuti sungakwanitsе kukhala alone yeah
umakopeka nzanga, umabalalika msanga
umakopeka nzanga

[chorus]
simuchedwa kugwa, simuchedwa kulola
m’makonda zachikunja
muposte pa status bola
akakutchula honey sweetie
(umakhala watheka) eh eh hee eh
akati tik*mana liti
(umakhala watheka) oooh oooh
simuchedwa kugwa, simuchedwa kulola
m’makonda zachikunja
muposte pa status bola
akakutchula honey sweetie
(umakhala watheka) eh eh hee eh
akati tik*mana liti
(umakhala watheka) oooh oooh

[outro]
simuchedwa kugwa, simuchedwa kulola
m’makonda zachikunja
muposte pa status bola
simuchedwa kugwa, simuchedwa kulola
m’makonda zachikunja
muposte pa status bola

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...