tempolale - eli njuchi lyrics
[intro]
hihihihiihihi o*obk beats baby
[verse 1]
baby don’t worry
usamadandaule
usamakaikire
masikuwa, uzilemba mu diary
mavutowa ndi history
zonsezi nzakalekale
chonde usazaiwale
masikuwa, uzilemba mu diary
[chorus]
zonsezi nza tempolale
tempolale
tempolale
masikuwa, uzilemba mu diary
zonsezi nza tempolale
mavuto athuwa nga, (tempolale)
misonzi yathuyi nja, (tempolale)
masikuwa, uzilemba mu diary
[verse 2]
koophya tadutsa kale, my lover
zachuma tamuk*mbukire yobu, my lover
zamwana tamuk*mbukire sarah, my…
amalanda amapatsa osaiwala, my lover
taona zambiri kufika lero, my lover
nde ulova nkachani?, my lover
kusowa ya rent nkachani?, my lover
kusowa ma fees nkachani?, my lover
[chorus]
zonsezi nza tempolale
mavuto athuwa nga, (tеmpolale)
misonzi yathuyi nja, (tempolale)
masikuwa, uzilеmba mu diary
zonsezi nza tempolale
mavuto athuwa nga, (tempolale)
misonzi yathuyi nja, (tempolale)
(oh*oh) masikuwa, uzilemba mu diary
[bridge]
olo mdima uophye bwanji
kunja kucha
namondwe aombe bwanji
tidzaoloka
iwe ndi ine
iwe ndi ine
olo mdima uophye bwanji
kunja kucha
namondwe aombe bwanji
tidzaoloka
iwe ndi ine
iwe ndi ine
[chorus]
zonsezi nza tempolale
tempolale
tempolale
masikuwa, uzilemba mu diary
zonsezi nza tempolale
mavuto athuwa nga, (tempolale)
misonzi yathuyi nja, (tempolale)
masikuwa, uzilemba mu diary
[outro]
hihihihiihihi o*obk beats baby
Random Song Lyrics :
- dear house - the ex (punk band) lyrics
- ceros a tu alma - teorico lyrics
- madlien - mitsuruggy lyrics
- secluded - q. villa lyrics
- scared of boys - char chris lyrics
- 50 - k$upreme lyrics
- high note - mark manthei lyrics
- wie du guckst - elo314 lyrics
- io ti penso - nyvinne lyrics
- se te enfrió el té - ignacio figueroa lyrics