usandipope - dirty flo lyrics
[intro : dirty flo & crispy malawi]
f9ine entertainment
brr! gang, gang, gang, gang, gang
yoh dirty, dirty, dirty
yeah spe, spe, spe
[verse 1: dirty flo & crispy malawi]
kufika kupanga attack ndi defence (ma dolo!)
the fans say i drive her crazy, ali ku chiphedi
ma jam alipo kale tungosaka bread
jah, jah waflippa ma odds, hater waluza bet
[chorus: crispy malawi & dirty flo]
usandipope choncho ndisazimve (mmh hm)
ngati zisali za ndalama ndisazimve (ayi)
uzipereka ndikokoma sindingagive (no way)
zimangofunika ku wekha ndi khalidwe (khalidwe)
yeah
usandipope choncho ndisazimve
ngati zisali za ndalama ndisazimve
uzipereka ndikokoma sindingagive (no way)
zimangofunika ku wekha ndi khalidwe (khalidwe)
[verse 2: crispy malawi & dirty flo]
don’t tell me what to do (to do)
ndili ndi dirty, hater ndikuthila doom (fefe)
ndili mu zone, ndayika baskеt (zone) (basket)
ndimapusha ngati ndine advеrt (advert)
i got the juice ngati nanchesi (juice, juice)
ku runner dancehall ngati advert
takudutsa ngati passage
tungosakaso zi money
kufuna ku baller ndi a’bale
nane i got goals, ndeno sindingakuseve
yeah i look alive komano ndafa ndiphwete (hahaha)
ndingo chiller ndi ziwindi ndili mkati chani
mfana woti ndinavaya osakutsanzikani
nde ka landlord kanu kaja kamati chani?
super glue with the game mati mati chani?
ndinaba game f*kwa ndinalibe game
ndili[?]
mfana sangandigunde pss, i left them hangin’
[chorus: crispy malawi & dirty flo]
usandipope choncho ndisazimve (ooh oh)
ngati zisali za ndalama ndisazimve (ndisazimve) (uh)
kuzipereka ndikokoma sindingagive (no, no)
zimangofunika ku wekha ndi khalidwe (khalidwe)
usandipope choncho ndisazimve (ndisazimve)
ngati zisali za ndalama ndisazimve (ndisazimve)
uzipereka ndikokoma sindingagive (uh, huh)
zimangofunika ku wekha ndi khalidwe (eeh, eeh)
[outro: dirty flo]
uh, huh, huh, uh, huh, uh, huh
uh, huh, huh,uh, huh, uh, huh
Random Song Lyrics :
- capital - gk silverr lyrics
- freiza - lil loak lyrics
- rocket mind - direlake lyrics
- ogni mai più - brenneke lyrics
- brechen - naif (rapper) lyrics
- biću njegova, izvini - sanela sijercic lyrics
- losing it - clayton shay lyrics
- kasca - cdzeta lyrics
- a drone opting out of the hive - code orange lyrics
- i don't wanna understand - taylor austin dye lyrics