lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

rara - dali citty lyrics

Loading...

[intro]
mo beats
titani poti ndiwe chi makina
wandipangitsa kupyeleza mang’ina
thupi banging ukuwoneka chi stamina
wandipangitsa kupyeleza (chux) kanyenya
tipatse plan

[verse 1]
nakuwuzapo
looks yako imandidololala
siza chipako
kutuluka ndamenya pula
i wanna see your face
come to my place i
wanna show you things i
have plans for you baby

[chorus]
rara
mmh rara
rara
mmh rara
titani poti ndiwe chi makina
wandipangitsa kupyeleza mang’ina
thupi banging ukuwoneka chi stamina
wandipangitsa kupyeleza kanyenya
hm hm hm hmm
you are driving me mad insane
[verse 2]
mami ooh mami ooh mami sindingakhale
mami ooh mami ooh chonchi sindingakhale
you got the coating
i got the mountain that you are the one mmh
your body nice made
you got the vibe got me falling
sindichitira mwina ndikusintha dzina
sindifunaso wina pano pavuta

[chorus]
rara
mmh rara
rara
mmh rara
titani poti ndiwe chi makina
wandipangitsa kupyeleza mang’ina
thupi banging ukuwoneka chi stamina
wandipangitsa kupyeleza kanyenya
hm hm hmm

[bridge]
(tabwela kuno ndikuwuze chinsisi)[?]
(tandipatse kiss ,skirt yako itsitse)
(ukhale pa easy)
[?]
[chorus]
rara
rara ooh
titani poti ndiwe chi makina
wandipangitsa kupyeleza mang’ina
thupi banging ukuwoneka chi stamina
wandipangitsa kupyeleza kanyenya

[outro]
titani poti ndiwe chi makina
wandipangitsa kupyeleza mang’ina
thupi banging ukuwoneka chi stamina
wandipangitsa kupyeleza kanyenya

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...