nyimbo - dali citty & jeff nyimbo lyrics
[intro]
(umanditengetsa)
(ukatengeza)
(umandipembedza)
(umandipengetsa)
(umanditengetsa)
(ukatengeza[?])
(umandipembedza)
(umanditentetsa)
(umandipengetsa)
tipatse plan
[chorus:dali]
wona baby ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
wandipengetsa ndakuyimbira nyimbo (nyimbo)
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo(nyimbo)
[post chorus : dali]
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi gitala
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi ma gitala
yeah
[verse 1: dali]
kukongola kukongola ku sipanja pokha
kukongola ndi mtima womwe
tasendera tasendera pafupi nane
ndifuna uwone
(umanditengetsa)
(ukatengeza)
(umandipembedza)
(umandipengetsa)
(umanditengеtsa)
(ukatengeza[?])
(umandipembеdza)
(umanditentetsa)
(umandipengetsa)
[chorus: dali]
wona baby ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
wandipengetsa ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
[post chorus : dali]
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi gitala
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi ma gitala
[verse 2: jeff nyimbo]
zoti uli kutali sizindikudza
akazi ena sandisuntha
sindiwafuna
ukamasekelera ineso ndimawonetsa mano
ichi ndichi mvano maso ayamba mwano
nde ndabwera ndi gitala (mmh)
sitisiyana (pengetsa) mpaka umvere nyimbo yanga (nyimbo yanga)
ukamadzuka utchole dance (utchole dance)
kugwedeza mtima w*nga momwe (utchole dance) umagwedezera (utchole dance)
[chorus: dali]
wona baby ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
wandipengetsa ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
[post chorus : dali]
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi gitala
sindifunika kulemba kalata
olo kuyimba foni
ndabwera ndi ma gitala
yeah
[bridge]
fire ooh
fire ooh
fire ooh
fire ooh
fire
ooh fire
girl you got me burning
burning by your fire
turn up your radio
when you hear this song
ndayimbira iwe
sindifunika kuyimba phone
turn up your radio
when you hear this song
ndayimbira iwe
[outro:dali]
ona baby ndakuyimbira nyimbo
nyimbo
ndakuyimbira nyimbo
Random Song Lyrics :