lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

ankolo - daddy xray lyrics

Loading...

(intro)

yeah!!! (groovy boy records)
okay!!! eeh!!
the x*ray gang

(pre hook)

ndilibe dollar ndimakhala kape (alright)
kuona nzanga aliyense akupanga zake (okay!!)
umva aise* (yeah!!) usatitsate ( yeah)
dollar tilibe zoti tingak*mwese
zikangolowa umva

(hook)
ankolo ankolo ankolo ( ankolo!!)
ankolo ankolo ankolooo aah ( yeah ankolo!!)
ankolo ankolo ankolo (grr ankolo)
ankolo* (alright) ankolo uh huh (alright)

(vs 1)

amalawilira phone yeah he!! (mmati bwanj?)

mmati ndikupatse moni yeah he!

ndamva zalowa ( it’s lit) man tipatseni plan yah huh! (aaah ndilibe kanthu)

musamaumile money eh heh! (straight up)

kupeza 2 mina mina kuzamva odi pa door (eeh! ndindani?)

ankolo tsegulani ndabweranso ndi bro (alright)

tapeza spot inayake k*meneko tikayaka bho(okay)

mukangogula mikunda (okay) tizika chaser ndi coco

pre hook)
ndilibe dollar ndimakhala kape (alright)
kuona nzanga aliyense akupanga zake (okay!!)
umva aise* (yeah!!) usatitsate ( yeah)
dollar tilibe zoti tingak*mwese
zikangolowa umva

(hook)

ankolo ankolo ankolo ( ankolo!!)
ankolo ankolo ankolooo aah ( yeah ankolo!!)
ankolo ankolo ankolo (grr ankolo)
ankolo* (alright) ankolo uh huh (alright)

(vs2)

dollar zanga ndapangila pachiseko(okay) undiuza bwanj makona(yeah)

tikudziwa ndiwe nzanthu koma ndiwe m’bale tikamakuona(okay)

inu ndi chadwick (u yeah) eya inu ndinu boseman

nkatenge chan? mungotigulira umodzi okha (okay)

kenako basi (yeah!)

kuumwa kenako dance (yeah)
kucha kenako frus (it’s lit)

ndilibe kanthu ndamwesa ma braz (okay)

m’mawa ndilibe kanthu (wooh)

kuchita kusowa ya bundle (gang gang)

kuwa caller sakuyankhanso

amandipatsa moto ndisakuyakanso

ati aseh xray ndiwaukape(okay)

ati lero alibe kanthu ndiyeno tikamumwetse (quan boy)

aaah! asatibhowe tyeko tingom*th*wa(alright)

akakhala ndi dollar zambiri tiye tizingozithaaa!

pre hook)

ndilibe dollar ndimakhala kape (alright)
kuona nzanga aliyense akupanga zake (okay!!)
umva aise* (yeah!!) usatitsate ( yeah)
dollar tilibe zoti tingak*mwese
zikangolowa umva

(hook)

ankolo ankolo ankolo ( ankolo!!)
ankolo ankolo ankolooo aah ( yeah ankolo!!)
ankolo ankolo ankolo (grr ankolo)
ankolo* (alright) ankolo uh huh (alright)

(outro)

ankolo ankolo ankolo
ankolo ankolo ankolooo aah
ankolo ankolo ankolo
ankolo* ankolo uh huh

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...