uzithamanga - crispy malawi lyrics
[intro]
ayo landie
uzithamanga (huh huh)
uzithamanga (hmm hmm)
uzithamanga (iwe uyo)
uzithamanga (ay)
[pre*chorus]
si iwe hule sizomango gona ku kacha (ku culture!)
uzidzuka uzi thamanga thamanga
sizomangolira ngati mwana ukagwa (ngaa)
ukadzuka kusasa fumbi k*mathanga
utha kusuta kuti ugainy confi (ha)
koma bola osathamanga
sungathamange madzi atafika mkhosi (ha)
nde olo apapa ukhozano kungoyamba
kuthamanga (rah)
[chorus]
k*mathanga (go!)
uzithamanga (uh huh)
uzithamanga
uzithamanga (huh)
[verse]
k*ma talker promoter sindimadya exposure
ati eh spe unatha mantha (k*mene)
za ulere sindikupanga olo kamodzi
mmmh man bolani kupanga zanga (amen)
olo mpamba ine nditha kupatsa (eh heh)
koma ukasanja umapanga zotasa (zoba)
ine ndimapanga zomwe ndimafuna
iwe umalandira zomwe amakupasa (ceo)
basi busy mu hood kuzimva ushasha (zoba)
mafana opepela osadziwa ku hasa (zoba)
business idea kuphwekesa mogo k*mapemphesa
ana amu hood kuwawopyeza
[chorus]
uzithamanga
uzithamanga (iwe)
uzithamanga
uzithamanga
[pre*chorus]
si iwe hule sizomango gona ku kacha (ku culture)
uzidzuka uzi thamanga thamanga (aaah ase!)
sizomangolira ngati mwana ukagwa (ngaa)
ukadzuka kusasa fumbi k*mathanga (sa sa sa sa sa)
utha kusuta kuti ugainy confi (huh)
koma bola osathamanga (osa ng’aza)
sungathamange madzi atafika mkhosi (huh)
nde olo apapa ukhozano kungoyamba
kuthamanga
[chorus]
k*mathanga (rah)
uzithamanga (hu)
uzithamanga (hu)
uzithamanga (hu)
Random Song Lyrics :
- power of soul - live at fillmore east 12/31/1969 - jimi hendrix lyrics
- inseguranças - jovem jaune lyrics
- undress to confess - powerwolf lyrics
- hey baby - bubble guppies cast lyrics
- can't take away - jeremy camp lyrics
- nach hos deg - slæm dønk lyrics
- xan’t let it ride ft. boosie - bop menaxe lyrics
- frost - spaceghostpurrp lyrics
- written - dana jean phoenix lyrics
- i dream of you - seo sung hyuk (서성혁) lyrics