lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

pantalonè - crispy malawi lyrics

Loading...

[intro: crispy malawi]
uh*huh uh*huh
uh*huh uh*huh uh*huh
tsono nzawinner [?]
okay

[chorus: crispy malawi]
praise the lord
nduwoneka bho ndavala pant alone (uh*huh)
met my ex akuti “mmh you’ve changed a lot”
the grind don’t stop ’till you see the benz on the parking lot

[verse 1: crispy malawi]
i had no where to go, big bro didn’t like my smokin’ habits (habits)
pano blessings ndi nyanja ngati ndimagona mkachasi (mkachasi)
hit me up pa den uli ndi ufulu wof*kisa tchalisi (tchalisi)
koma fwaka ndi panja f*kwa mkati muno nalesa
utha kulinka ndi eli njuchi ngati ufuna malesa (malesa)
anthu ena amatha kusintha city utawatenga ku dedza (ku dedza)
koma usazaf**ke uzizapusha uzabooleza (uzabooleza)
ngati siwe jah jah uli panja sindupembedza (sindupembedza)
pamalo timatenthetsa (timatenthetsa), matako amagwedeza
so many fishes in the sеa, koma uziwa dollar ndi m’bedza
i wanna get back to my [?] kuti azandiyike mu gеneza[?]
ife timafilidwa ndi ana chif*kwa timabhebhetsa
sizachisinsi tiku chaser milli (mili mili)
tikayipeza kuyipanga yambirimbiri (mbiri mbiri)
numbers goin’ crazy ndati muyimbire phini
tizaflipe milli tinapanga mili (mili mili)
mhu mhu
tinapanga mbiri (mbiri mbiri)
[chorus: crispy malawi]
praise the lord
nduwoneka bho ndavala pant alone
met my ex akuti “mmh you’ve changed a lot”
the grind don’t stop ’till you see the benz on the parking lot

[verse 2: brainlock boi sticx]
fresh out the chat[?] ndili*
fresh out the chat ndili drunk and high
highschool kid ndatopa ndikudya ma pie[?]
dm sindiyankha hie
don’t wonder why most people who do that
amapanga waste my time
mkazi wako amafuna azindikhalira pama thighs
ndakakisser kati ndik*mveka gin kalindi breathalyzer
kakuti “bwanji sumapanga condomize?”
ndati “ndinapanga circumcise”
ndati “ndinapanga circumcise”
ndati “ndinapanga circumcise”
ndati “ndinapanga circumcise”
ndati “ndinapanga circumcise”
ndati “ndinapanga circu” ah

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...