lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

benz - crispy malawi lyrics

Loading...

[intro]
dem baad
dem baddies
yeah

[chorus]
lisa amandibalalisa
mercy akuti sangadyese
jesse akati agwedeze
utha ku spenda ndalama zonse
praise akufunika benz
aggie akufunika kheshi
ya i phone, nails ndima ma mesh
ndi blessor oti azilipira rent
ine benz, ndikufunika benz
benz, ndikufunika benz
benz, ndikufunika benz
benz ndikufuna benz

[verse]
ndi good girl amangofuna vepi
ma bwana amangomutsitsa dress
nde friend akuvaila nurse
kuti azingophaka plain
muzifunsa musanapange date
mandem anagwira nazo ex
ataziwa *n*li ndima stress
nde anangoyamba ku hater wеzi wezi
dollar zanu osamangomwera best
zina k*mapangako invеst
more profits, kuchepesa ma regrets
kuchulusa ma returns

[chorus]
lisa amandibalalisa
mercy akuti sangadyese
jesse akati agwedeze
utha ku spenda ndalama zonse
praise akufunika benz
aggie akufunika kheshi
ya i phone, nails ndima ma mesh
ndi blessor oti azilipira rent
ine benz, ndikufunika benz
benz, ndikufunika benz
benz, ndikufunika benz
benz ndikufuna benz

[outro]
ndikufunika benz
ndikufuna benz

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...