lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

yoghurt - crispy malawi & 60 grxmz lyrics

Loading...

[chorus: crispy malawi]
sungandisaize dancehall ina sintha singatalker sunathayime
i got some m’s in the bank koma sindingakunyaditse
ma cheese nde ndi nyanja koma sindinga*
sindingakubanditse
sindingakubanditse
sindingakubanditse
sindinga*

[verse 1: crispy malawi]
ndiwe mfana woseketesa heavy sungandikwiyitse
ndili ndi chimwana chi beyoncé sungachithayime
iwe spe sakufunika dzuwa kuti ashine
wavala watch ya bho koma ino ndi nthawi ya ine
palibepo baddie pa schedule pa ine
koma utha kundi hitter ngati ndili online
osandifunsa kuti ndingoyankha “i’m fine”
mpatse mita mandingo azayike pipe

[verse 2: 60 grams]
ndungofila bho, smokey wabwera pa benz
me and boys workin’ palibepo za ulesi
you gotta lean after nangodyela cheese
they keep sayin’ i’m crazy, told them that phin is my gee
can’t mess with me mafana ndine wa street
i’m high on can’t give no attention to a b*tch
si iwe dolo ngati umalimbana ndine
mafana a ulesi kukonda kupatsa busy
[chorus: crispy malawi]
sungandisaize dancehall ina sintha singatalker sunathayime
i got some m’s in the bank koma sindingakunyaditse
ma cheese nde ndi nyanja koma sindinga*
sindingakubanditse
sindingakubanditse
sindingakubanditse
sindinga*

[outro: crispy malawi]
ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty
ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty
ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...