lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

witchu - brainlock kushizzo lyrics

Loading...

it’s you that mega

[chorus]
i just wanna be witchu
usandiyikiletu panja
tizipanga zathu
imma call you ndikasanja
i just wanna be witchu
usandiyikiletu panja
tizipanga zathu
imma call you ndikasanja

[verse 1]
uwu ulendo wautali uwu tandigwire mkono
sindimvetsa from the dizzo eya ndaona zikh0m*
maso anga patsogolo eya mbuyo sunduyan’ganako
osalora anzakowo akulande hustle yako
say lose ilipo [?] mutu umagwira
nthawi ikubwera sinzatopa kudikira
plan yanzeru ndili nayo osandikayira
once i get the door naweso nzakupakulira
ndingofuna kukhale nawe
osalora munthu wachitatu asokoneze ngini yathu ndi anthu two
osamawamvera ndi ma hater akathoka
angolongolora ngati mpututhu
[chorus]
i just wanna be witchu
usandiyikiletu panja
tizipanga zathu
imma call you ndikasanja
i just wanna be witchu
usandiyikiletu panja
tizipanga zathu
imma call you ndikasanja

[verse 2]
sindimakuyiwala ndikasanja
nanga dollar ya show iyi ndizidya ndi ndani?
ndimakuyimbira ukaflasher
tilipa awiri ukundivula shati
tiye ku trap ukayiziwe gang
umakhala mumtima mw*nga osapayer rent
ukhale mbali yanga usaswitche ngati kasefi
kusiyana ndi shizzo uzapanga n*z* regret
sindingalore uzivutika ndili bho
imma spend my monеy witchu mthumba mukakhala bho
ukakhala wandisowa uzingo ndimenyera call
ndimakhala busy kuyimba nyimbo mu studio

[chorus]
i just wanna be witchu
usandiyikilеtu panja (panja)
tizipanga zathu (zathu zathu)
imma call you ndikasanja (racks)
i just wanna be witchu (witchu witchu)
usandiyikiletu panja (panja)
tizipanga zathu (zathu zathu)
imma call you ndikasanja (sanja)
[outro]
i just wanna be witchu
usandiyikiletu panja (panja)
tizipanga zathu (zathu zathu)
ama call you ndikasanja (racks)
i just wanna be witchu (witchu witchu)
usandiyikiletu panja (panja)
tizipanga zathu (zathu zathu)
ama call you ndikasanja (sanja)

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...