july - brainlock kushizzo lyrics
[intro]
it’s prodogy
[chorus: kushizzo & nkhiwa]
pepani nakusiyani mukudikira
koma tape ina nditulutsa mu july
ndili mu stu nyimbo ndikujudula
kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
kufuna ndizingokuona uk*mwetulira (lira aah)
uzindiwuza ndizipanga mene ukufunira (ukufunira aah)
osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
[verse 1: nkhiwa]
kodi mumva round (ooo oo) m’mamva ngati andigwira
pano full sight ndik*maona njira (ooo oo)
ukhale ndi good vibes ukandiyandikira (aah ah)
shawty not my koma ak*mandipatsira (ooo oo)
titulutsa nyimbo zina chamu july
nkhiwa ndi kushizzo ndima trap or die
kuodetsa chi two litre kungonyombeka
(ooo oo) khalifa alikutiko? sakuwoneka
this music for my fan (ooo oo), i’m on zero
she a rich b*tch she dance ,samatha kugwira nthiko (ooo oo)
nyimbozo in my plan , tikugwira ntchito (ooo oo)
koma osadanda fam mumvera zi nyimbo
[chorus: kushizzo & nkhiwa]
pepani nakusiyani mukudikira
koma tape yina nditulutsa mu july
ndili mu stu nyimbo ndikujudula
kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
kufuna ndizikuona uk*mwetulira (mwetulira aah)
uzindiwuza ndizipanga mene ukufunira (ukufunira aah)
osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
[verse 2: kushizzo & nkhiwa]
sukufulumira ngati ukusochera (ukusochera)
njira nzosiyana komwe tikulowera (tikulowera)
ndinali pansi koma pano ndazitolera (ndazitolera)
ndimangopanga utsi pano nde ndakolera (ndakolera)
ndatenga malo ndatenga bics
ndinapanga strategize ona blueprint (blueprint)
akudabwa ma ghost kupanga achieve
sinanga ankaphweketsa and we still had to believe
see me pull on a whip (whip), ndikufuna kupusher whip
see me on tv (tv) musandisowe kwambiri (kwambiri)
utha kutenga pic tikak*mana mu street (mu street)
ndikupanga izizi chif*kwa fanz ndimakukondani
[chorus: kushizzo & nkhiwa]
pepani nakusiyani mukudikira (mukudikira)
koma tape ina nditulutsa mu july (mu july)
ndili mu stu nyimbo ndikujudula (kujudula)
kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
kufuna ndizikuona uk*mwetulira (mwetulira aah)
uzindiwuza ndizipanga mene ukufunira (ukufunira aah)
osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
pepani nakusiyani mukudikira (mukudikira)
koma tape ina nditulutsa mu july (mu july)
ndili mu stu nyimbo ndikujudula (kujudula aah)
kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
kufuna ndizikuona uk*mwetulira (mwetulira aah) (it’s prodogy)
uzindiwuza ndizipanga mene ukufunira (ukufunira aah)
osandinyoza pano moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
Random Song Lyrics :
- consequence - skold lyrics
- castle in the clouds - etza meisyara lyrics
- sarajlija - crvena jabuka lyrics
- kima nina كيما - itskoast lyrics
- losing my mind - elliatzo lyrics
- nothing 2 lose - ely waves & chrispyd & jauque x lyrics
- elikya (mouvement historique #5) - frenetik (bel) lyrics
- tough love - majeeed lyrics
- take my hand - trinah lyrics
- советчик (adviser) - сеня андронов (senja andronov) lyrics